Yesaya 62:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma iwo amene adzakolola adzadya ndi kutamanda Yehova; ndi iwo amene adzamchera adzamumwa m'mabwalo a kacisi wanga.

Yesaya 62

Yesaya 62:7-11