Yesaya 62:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, Yehova walalikira kufikira malekezero a dziko lapansi. Nenani kwa mwana wamkazi wa Ziyoni, Taona cipulumutso cako cifika; taona mphotho yace ali nayo, ndi nchito yace iri pamaso pace.

Yesaya 62

Yesaya 62:2-12