Yesaya 61:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Ine Yehova ndikonda ciweruziro, ndida cifwamba ndi coipa; ndipo ndidzawapatsa mphotho yao m'zoonadi; ndipo ndidzapangana nao pangano losatha.

Yesaya 61

Yesaya 61:1-11