Yesaya 60:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Dzuwa lako silidzalowanso, mwezi wako sudzanka kumidima; pakuti Yehova adzakhala kuunika kwako kosatha, ndi masiku a kulira maliro ako adzatha.

Yesaya 60

Yesaya 60:18-22