Yesaya 60:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti taona, mdima udzaphimba dziko lapansi, ndi mdima wa bii mitundu ya anthu; koma Yehova adzakuturukira, ndi ulemerero wace udzaoneka pa iwe.

Yesaya 60

Yesaya 60:1-10