Yesaya 60:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwe udzayamwanso mkaka wa amitundu, nudzayamwa bere la mafumu, nudzadziwa kuti Ine Yehova ndine mpulumutsi wako, ndi Mombolo wako, Wamphamvu wa Yakobo.

Yesaya 60

Yesaya 60:6-21