Yesaya 60:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zipata zako zidzakhalabe zotseguka, sizidzatsekedwa usana pena usiku, kuti abwere naco kwa iwe cuma ca amitundu, ndi mafumu ao otsogozedwa nao pamodzi.

Yesaya 60

Yesaya 60:6-12