Yesaya 6:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ine ndinati, Tsoka kwa ine! cifukwa ndathedwa; cifukwa ndiri munthu wa milomo yonyansa, ndikhala pakati pa anthu a milomo yonyansa; cifukwa kuti maso anga aona Mfumu, Yehova wa makamu.

Yesaya 6

Yesaya 6:1-6