Yesaya 6:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pompo ndinati ine, Ambuye mpaka liti? Ndipo anayankha, Mpaka midzi ikhala bwinja, yopanda wokhalamo, ndi nyumba zopanda munthu, ndi dziko likhala bwinja ndithu,

Yesaya 6

Yesaya 6:1-12