Yesaya 59:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco iwo adzaopa dzina la Yehova kucokera kumadzulo, ndi ulemerero wace kumene kuturukira dzuwa; pakuti pamene mdani adzafika ngati cigumula, mzimu wa Yehova udzamkwezera mbendera yomletsa.

Yesaya 59

Yesaya 59:9-21