Yesaya 59:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye anaona kuti palibe munthu, nazizwa kuti palibe wopembedzera; cifukwa cace mkono wace wace unadzitengera yekha cipulumutso; ndi cilungamo cace cinamcirikiza.

Yesaya 59

Yesaya 59:6-17