Yesaya 58:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, inu musala kudya kuti mukangane ndi kutsutsana ndi kukantha ndi nkhonya yoipa; inu simusala kudya tsiku lalero kuti mumveketse mau anu kumwamba.

Yesaya 58

Yesaya 58:1-11