Yesaya 57:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti pa miyala yosalala ya m'cigwa pali gawo lako; iyo ndiyo gawo lako; ndiyo imene unaitsanulirira nsembe yothira, ndi kupereka nsembe yaufa. Kodi ndidzapembedzedwa pa zinthu zimenezi?

Yesaya 57

Yesaya 57:5-16