Yesaya 55:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

woipa asiye njira yace, ndi munthu wosalungama asiye maganizo ace, nabwere kwa Yehova; ndipo Yehova adzamcitira cifundo; ndi kwa Mulungu wathu, pakuti Iye adzakhululukira koposa.

Yesaya 55

Yesaya 55:1-13