Yesaya 55:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Bwanji inu mulikutayira ndarama cinthu cosadya, ndi kutayira malipiro anu zosakhutitsa? Mverani Ine mosamalitsa, nimudye cimene ciri cabwino, moyo wanu nubondwere ndi zonona.

Yesaya 55

Yesaya 55:1-6