Yesaya 55:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

momwemo adzakhala mau anga amene aturuka m'kamwa mwanga, sadzabwerera kwa Ine cabe, koma adzacita cimene ndifuna, ndipo adzakula m'mene ndinawatumizira.

Yesaya 55

Yesaya 55:1-13