Yesaya 54:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti iwe udzafalikira ponse pa dzanja lamanja ndi lamanzere, ndipo mbeu yako idzalandira amitundu colowa cao, ndi kukhalitsa anthu m'mabwinja.

Yesaya 54

Yesaya 54:1-4