Yesaya 54:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'cilungamo iwe udzakhazikitsidwa, udzakhala kutari ndi cipsinjo, pakuti sudzaopa; udzakhala kutari ndi mantha, pakuti sadzafika cifupi ndi iwe.

Yesaya 54

Yesaya 54:4-17