Yesaya 53:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye ananyozedwa ndi kukanidwa ndi anthu; munthu wazisoni, ndi wodziwa zowawa; ndipo ananyozedwa monga munthu wombisira anthu nkhope zao; ndipo ife sitinamlemekeza.

Yesaya 53

Yesaya 53:1-7