Yesaya 52:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Dzisanse pfumbi; uka, khala tsonga, Yerusalemu; udzimasulire maunyolo a pakhosi pako, iwe mwana wamkazi wam'nsinga wa Ziyoni.

Yesaya 52

Yesaya 52:1-7