Yesaya 52:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti simudzacoka mofulumira, kapena kunka mothawa; pakuti Yehova adzakutsogolerani, ndi Mulungu wa Israyeli adzadikira pambuyo panu.

Yesaya 52

Yesaya 52:10-15