Yesaya 52:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova wabvula mkono wace woyera pamaso pa amitundu onse; ndi malekezero onse a dziko lapansi adzaona cipulumutso ca Mulungu wathu.

Yesaya 52

Yesaya 52:3-15