Yesaya 51:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mverani Ine, inu anthu anga, ndi kundicherera makutu, iwe, mtundu wa anthu anga; pakuti lamulo lidzacokera kwa ine, ndipo ndidzakhazikitsa ciweruziro canga cikhale kuunika kwa anthu.

Yesaya 51

Yesaya 51:3-8