Yesaya 51:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Izi ziwiri zakugwera; ndani adzakulira iwe? bwinja ndi cipasuko, njala ndi lupanga; ndidzatonthoza mtima wako bwanji?

Yesaya 51

Yesaya 51:13-23