Yesaya 51:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Galamuka, galamuka, imirira Yerusalemu amene unamwa m'dzanja la Yehova cikho ca ukali wace; iwe wamwa mbale ya cikho conjenjemeretsa ndi kucigugudiza.

Yesaya 51

Yesaya 51:8-23