Yesaya 51:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine, Inedi, ndine amene nditonthoza mtima wako; kodi iwe ndani, kuti uopa munthu amene adzafa, ndi mwana wa munthu amene adzakhala ngati udzu;

Yesaya 51

Yesaya 51:6-22