Yesaya 50:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ambuye Yehova wandipatsa Ine lilime la ophunzira, kuti ndidziwe kunena mau akucirikiza iye amene ali wolema. Iye andigalamutsa m'mawa ndi im'mawa, nagalamutsa khutu langa kuti limve monga ophunzira.

Yesaya 50

Yesaya 50:1-8