Yesaya 48:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inde, iwe sunamva; inde, sunadziwe; inde, kuyambira kale khutu lako silinatsegudwe; pakuti ndinadziwa kuti iwe wacita mwaciwembu ndithu, ndipo unayesedwa wolakwa cibadwire.

Yesaya 48

Yesaya 48:1-14