Yesaya 48:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Turukani inu m'Babulo, athaweni Akasidi; ndi mau akuyimba nenani inu, bukitsani ici, lalikirani ici, ngakhale ku malekezero a dziko; nenani, Yehova waombola mtumiki wace Yakobo.

Yesaya 48

Yesaya 48:16-22