Yesaya 48:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sonkhanani inu nonse ndi kumva, ndani mwa iwo aonetsa zinthu izi? Iye amene Yehova anamkonda, iye adzacita kufuna kwace pa Babulo, ndi mkono wace udzakhala pa Akasidi.

Yesaya 48

Yesaya 48:4-15