Yesaya 47:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinakwiyira anthu anga, ndinaipitsa colowa canga, ndi kuwapereka m'manja ako; koma iwe sunawaonetsera cifundo; wasenzetsa okalamba goli lako lolemera ndithu.

Yesaya 47

Yesaya 47:5-15