Yesaya 47:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti wakhulupirira zoipa zako, wati, Palibe wondiona ine; nzeru zako ndi cidziwitso cako zakusandutsa woipa; ndipo wanena mumtima mwako, Ndine, ndipo popanda ine palibenso wina.

Yesaya 47

Yesaya 47:1-13