Yesaya 45:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti anthu akadziwe kucokera ku maturukiro a dzuwa ndi kumadzulo, kuti palibe wina popanda Ine; Ine ndine Yehova, palibe winanso.

Yesaya 45

Yesaya 45:2-8