Yesaya 45:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndidzakupatsa iwe cuma ca mumdima, ndi zolemera zobisika za m'malo am'tseri, kuti iwe udziwe kuti Ine ndine Yehova, amene ndikuitana iwe dzina lako, ndine Mulungu wa Israyeli.

Yesaya 45

Yesaya 45:1-12