Yesaya 45:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yang'anani kwa Ine, mupulumutsidwe, inu malekezero onse a dziko; pakuti Ine ndine Mulungu, palibe wina.

Yesaya 45

Yesaya 45:12-25