Yesaya 44:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndani adzaitana monga Ine, ndi kulalikira ici ndi kundilongosolera ici, cikhazikitsire Ine anthu akale? milunguyo iwadziwitse zomwe zirinkudza, ndi za m'tsogolo.

Yesaya 44

Yesaya 44:1-16