Yesaya 44:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wina adzati, Ine ndiri wa Yehova; ndi wina adzadzicha yekha ndi dzina la Yakobo, ndipo wina adzalemba ndi dzanja lace, Ndine wa Yehova, ndi kudzicha yekha ndi mfunda wa lsrayeli.

Yesaya 44

Yesaya 44:4-7