Yesaya 44:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

atero Yehova, amene anakutenga iwe, nakuumba kucokera m'mimba, amene adzathangata iwe. Usaope Yakobo, mtumiki wanga ndi iwe, Yesuruni, amene ndakusankha iwe.

Yesaya 44

Yesaya 44:1-4