Yesaya 43:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine ndidzati ndi kumpoto, Pereka; ndi kumwera, Usaletse; bwera nao ana anga amuna kucokera kutari, ndi ana anga akazi kucokera ku malekezero a dziko lapansi;

Yesaya 43

Yesaya 43:1-10