Yesaya 43:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nyama za m'thengo zidzandilemekeza, ankhandwe ndi nthiwatiwa; cifukwa ndipatsa madzi m'cipululu, ndi mitsinje m'mkhwangwala, ndimwetse anthu anga osankhika;

Yesaya 43

Yesaya 43:14-24