Yesaya 43:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Mombolo wanu, Woyera wa Israyeli: Cifukwa ca inu ndatumiza ku Babulo, ndipo ndidzatsitsira iwo onse monga othawa, ngakhale Akasidi m'ngalawa za kukondwa kwao.

Yesaya 43

Yesaya 43:4-17