Yesaya 43:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine ndalalikira, ndipo ndikupulumutsa ndi kumvetsa, ndipo panalibe Mulungu wacilendo pakati pa inu; cifukwa cace inu ndinu mboni zanga, ati Yehova, ndipo Ine ndine Mulungu.

Yesaya 43

Yesaya 43:3-13