Yesaya 42:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo adzabwezedwa m'mbuyo, adzakhala ndi manyazi ambiri amene akhulupirira mafano osemedwa, nati kwa mafano oyengeka, Inu ndinu milungu yathu.

Yesaya 42

Yesaya 42:8-23