Yesaya 42:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndakhala nthawi yambiri wosalankhula; ndakhala cete ndi kudzithungata ndekha; tsopano ndidzapfuula ngati mkazi wobala; ndidzapuma modukizadukiza ndi wefuwefu pamodzi.

Yesaya 42

Yesaya 42:13-21