Yesaya 41:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndautsa wina wakucokera kumpoto; ndipo iye wafika wakucokera poturuka dzuwa, amene achula dzina langa; ndipo iye adzafika pa olamulira, monga matope, ndi monga muumbi aponda dothi la mbiya.

Yesaya 41

Yesaya 41:22-27