Yesaya 41:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Chulani zinthu zimene zirinkudza m'tsogolo, kuti ife tidziwe kuti inu ndinu milungu; inde, citani zabwino, kapena citani zoipa, kuti ife tiopsyedwe, ndi kuona pamodzi.

Yesaya 41

Yesaya 41:21-29