Yesaya 41:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Ine Yehova Mulungu wako ndidzagwira dzanja lako lamanja, ndi kunena kwa iwe, Usaope ndidzakuthandiza iwe.

Yesaya 41

Yesaya 41:8-14