Yesaya 39:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hezekiya anati kwa Yesaya, Mau a Yehova, amene iwe wanena, ali abwino. Iye anatinso, Pakuti padzakhala mtendere ndi zoonadi masiku anga.

Yesaya 39

Yesaya 39:1-8