Yesaya 39:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, masiku afika, kuti zonse za m'nyumba mwako, ndi zimene atate ako anazikundika kufikira lero lino, zidzatengedwa kunka ku Babulo; sipadzatsala kanthu, ati Yehova.

Yesaya 39

Yesaya 39:4-8