Yesaya 38:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pokhala panga pacotsedwa, pandisunthikira monga hema wambusa;Ndapindapinda moyo wanga ngati muomba;Iye adzandidula ine poomberapo;Kuyambira usana kufikira usiku mudzanditsiriza ine.

Yesaya 38

Yesaya 38:11-21